2 Mafumu 15:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Pamapeto pake, Hoshiya+ mwana wa Ela anakonzera chiwembu+ Peka mwana wa Remaliya n’kumupha.+ Kenako iye anayamba kulamulira m’malo mwake m’chaka cha 20 cha Yotamu+ mwana wa Uziya. 2 Mafumu 17:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 M’chaka cha 12 cha Ahazi mfumu ya Yuda, Hoshiya+ mwana wa Ela anakhala mfumu ya Isiraeli ku Samariya+ kwa zaka 9.
30 Pamapeto pake, Hoshiya+ mwana wa Ela anakonzera chiwembu+ Peka mwana wa Remaliya n’kumupha.+ Kenako iye anayamba kulamulira m’malo mwake m’chaka cha 20 cha Yotamu+ mwana wa Uziya.
17 M’chaka cha 12 cha Ahazi mfumu ya Yuda, Hoshiya+ mwana wa Ela anakhala mfumu ya Isiraeli ku Samariya+ kwa zaka 9.