2 Mafumu 18:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kenako anayamba kuitana mfumu mofuula, ndipo kunabwera Eliyakimu+ mwana wa Hilikiya amene anali woyang’anira banja lachifumu, Sebina+ mlembi, ndi Yowa mwana wa Asafu wolemba zochitika. Yesaya 22:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 “‘M’tsiku limenelo ndidzaitana mtumiki wanga+ Eliyakimu,+ mwana wa Hilikiya.+
18 Kenako anayamba kuitana mfumu mofuula, ndipo kunabwera Eliyakimu+ mwana wa Hilikiya amene anali woyang’anira banja lachifumu, Sebina+ mlembi, ndi Yowa mwana wa Asafu wolemba zochitika.