2 Mafumu 18:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kenako anayamba kuitana mfumu mofuula, ndipo kunabwera Eliyakimu+ mwana wa Hilikiya amene anali woyang’anira banja lachifumu, Sebina+ mlembi, ndi Yowa mwana wa Asafu wolemba zochitika. 2 Mafumu 18:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Koma Eliyakimu+ mwana wa Hilikiya amene anali woyang’anira banja lachifumu, Sebina+ mlembi, ndi Yowa+ mwana wa Asafu wolemba zochitika, anapita kwa Hezekiya atang’amba zovala zawo+ n’kumuuza mawu a Rabisake. Yesaya 36:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kenako kunabwera Eliyakimu+ mwana wa Hilikiya amene anali woyang’anira banja lachifumu, Sebina+ mlembi, ndi Yowa+ mwana wa Asafu+ wolemba zochitika.+
18 Kenako anayamba kuitana mfumu mofuula, ndipo kunabwera Eliyakimu+ mwana wa Hilikiya amene anali woyang’anira banja lachifumu, Sebina+ mlembi, ndi Yowa mwana wa Asafu wolemba zochitika.
37 Koma Eliyakimu+ mwana wa Hilikiya amene anali woyang’anira banja lachifumu, Sebina+ mlembi, ndi Yowa+ mwana wa Asafu wolemba zochitika, anapita kwa Hezekiya atang’amba zovala zawo+ n’kumuuza mawu a Rabisake.
3 Kenako kunabwera Eliyakimu+ mwana wa Hilikiya amene anali woyang’anira banja lachifumu, Sebina+ mlembi, ndi Yowa+ mwana wa Asafu+ wolemba zochitika.+