Yesaya 36:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kenako kunabwera Eliyakimu+ mwana wa Hilikiya amene anali woyang’anira banja lachifumu, Sebina+ mlembi, ndi Yowa+ mwana wa Asafu+ wolemba zochitika.+ Yesaya 36:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Koma Eliyakimu+ mwana wa Hilikiya amene anali woyang’anira banja lachifumu,+ Sebina+ mlembi, ndi Yowa+ mwana wa Asafu wolemba zochitika, anapita kwa Hezekiya atang’amba zovala zawo+ n’kumuuza mawu a Rabisake.+
3 Kenako kunabwera Eliyakimu+ mwana wa Hilikiya amene anali woyang’anira banja lachifumu, Sebina+ mlembi, ndi Yowa+ mwana wa Asafu+ wolemba zochitika.+
22 Koma Eliyakimu+ mwana wa Hilikiya amene anali woyang’anira banja lachifumu,+ Sebina+ mlembi, ndi Yowa+ mwana wa Asafu wolemba zochitika, anapita kwa Hezekiya atang’amba zovala zawo+ n’kumuuza mawu a Rabisake.+