Salimo 84:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Poyenda m’chigwa chouma mmene muli zitsamba za baka,*+Amasandutsa chigwacho kukhala choyenda madzi ochokera pakasupe,Mlangizi wafunda mawu otamanda.+ Salimo 107:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Amasandutsa chipululu kukhala dambo la madzi,+Ndipo dziko lopanda madzi amalisintha kukhala dera la akasupe amadzi.+
6 Poyenda m’chigwa chouma mmene muli zitsamba za baka,*+Amasandutsa chigwacho kukhala choyenda madzi ochokera pakasupe,Mlangizi wafunda mawu otamanda.+
35 Amasandutsa chipululu kukhala dambo la madzi,+Ndipo dziko lopanda madzi amalisintha kukhala dera la akasupe amadzi.+