Salimo 38:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pakuti ine ndikuyembekezera inu Yehova.+Inu Yehova Mulungu wanga, mudzandiyankha.+