2 Samueli 16:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Mwina Yehova aona+ ndi diso lake, ndipo lero Yehova abwezeretsa kwa ine zinthu zabwino m’malo mwa temberero la Simeyi.”+ Salimo 39:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Nanga tsopano, inu Yehova, ine ndikuyembekezera chiyani?Chiyembekezo changa chili mwa inu.+ Salimo 123:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Taonani! Monga mmene maso a atumiki amayang’anira dzanja la mbuye wawo,+Mmene maso a kapolo wamkazi amayang’anira dzanja la mbuye wake wamkazi,+Momwemonso, maso athu adzayang’ana kwa Yehova Mulungu wathu,+Kufikira atatikomera mtima.+
12 Mwina Yehova aona+ ndi diso lake, ndipo lero Yehova abwezeretsa kwa ine zinthu zabwino m’malo mwa temberero la Simeyi.”+
2 Taonani! Monga mmene maso a atumiki amayang’anira dzanja la mbuye wawo,+Mmene maso a kapolo wamkazi amayang’anira dzanja la mbuye wake wamkazi,+Momwemonso, maso athu adzayang’ana kwa Yehova Mulungu wathu,+Kufikira atatikomera mtima.+