Yesaya 10:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Nthawi iliyonse imene dzanja langa lafikira maufumu olambira milungu yopanda phindu, omwe zifaniziro zawo zogoba n’zambiri kuposa zimene zili ku Yerusalemu ndi ku Samariya,+
10 Nthawi iliyonse imene dzanja langa lafikira maufumu olambira milungu yopanda phindu, omwe zifaniziro zawo zogoba n’zambiri kuposa zimene zili ku Yerusalemu ndi ku Samariya,+