Yesaya 37:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Chifukwa anthu otsala adzachoka ku Yerusalemu,+ ndipo opulumuka adzachoka kuphiri la Ziyoni.+ Yehova wa makamu adzachita zimenezi modzipereka kwambiri.+
32 Chifukwa anthu otsala adzachoka ku Yerusalemu,+ ndipo opulumuka adzachoka kuphiri la Ziyoni.+ Yehova wa makamu adzachita zimenezi modzipereka kwambiri.+