-
2 Samueli 10:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Zitachitika zimenezi, Davide anati: “Ndidzasonyeza Hanuni mwana wa Nahasi kukoma mtima kosatha,+ monga mmene bambo ake anandisonyezera kukoma mtima kosatha.” Chotero Davide anatumiza uthenga kudzera mwa atumiki ake+ kuti akatonthoze Hanuni chifukwa cha imfa ya bambo ake, ndipo atumiki a Davidewo anafika m’dziko la ana a Amoni.
-