Salimo 37:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Munthu woipa amakongola zinthu za ena koma osabweza,+Koma wolungama amakomera mtima ena ndipo amapereka mphatso.+ Aroma 13:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Anthu inu musamakhale ndi ngongole iliyonse kwa munthu aliyense,+ kusiyapo kukondana,+ popeza amene amakonda munthu mnzake wakwaniritsa chilamulo.+
21 Munthu woipa amakongola zinthu za ena koma osabweza,+Koma wolungama amakomera mtima ena ndipo amapereka mphatso.+
8 Anthu inu musamakhale ndi ngongole iliyonse kwa munthu aliyense,+ kusiyapo kukondana,+ popeza amene amakonda munthu mnzake wakwaniritsa chilamulo.+