Genesis 21:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Ndiye chifukwa chake iye anatcha malowo Beere-seba,+ chifukwa chakuti onse awiri analumbirirana pamalopo. 1 Mafumu 19:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Choncho Eliya anachita mantha moti ananyamuka n’kuyamba kuthawa kuti apulumutse moyo wake,+ mpaka anakafika ku Beere-seba+ wa ku Yuda.+ Mtumiki wake anamusiya kumeneko,
31 Ndiye chifukwa chake iye anatcha malowo Beere-seba,+ chifukwa chakuti onse awiri analumbirirana pamalopo.
3 Choncho Eliya anachita mantha moti ananyamuka n’kuyamba kuthawa kuti apulumutse moyo wake,+ mpaka anakafika ku Beere-seba+ wa ku Yuda.+ Mtumiki wake anamusiya kumeneko,