Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 2:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Patapita nthawi, Farao anaimva nkhaniyi ndipo anafuna kupha Mose.+ Koma Mose anam’thawa+ Farao ndipo anapita kukakhala kudziko la Midiyani.+ Atafika kumeneko, anakhala pachitsime.

  • 1 Samueli 27:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Koma Davide anati mumtima mwake: “Tsiku lina Sauli adzandipha ndithu. Palibe chimene ndingachite choposa kuthawira+ kudziko la Afilisiti.+ Ndiyeno Sauli adzagwa ulesi ndipo adzasiya kundifunafuna m’dziko lonse la Isiraeli.+ Pamenepo ndidzakhala nditapulumuka m’manja mwake.”

  • Miyambo 16:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Mkwiyo wa mfumu umatanthauza amithenga a imfa,+ koma munthu wanzeru ndi amene amauziziritsa.+

  • Miyambo 22:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Wochenjera ndi amene amati akaona tsoka amabisala,+ koma anthu osadziwa zinthu amangopitabe ndipo amalangidwa.+

  • Mateyu 10:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Akakuzunzani mumzinda wina, muthawire mumzinda wina,+ pakuti ndithu ndikukuuzani, simudzamaliza kuzungulira+ mizinda yonse ya Isiraeli Mwana wa munthu asanafike.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena