1 Mafumu 14:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Iye adzasiya Isiraeli+ chifukwa cha machimo amene Yerobowamu anachita, ndiponso amene anachimwitsa nawo Isiraeli.”+ 1 Mafumu 15:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Izi zinachitika chifukwa cha machimo amene Yerobowamu anachita,+ ndiponso amene anachimwitsa nawo Isiraeli, komanso chifukwa cha zinthu zokwiyitsa Yehova Mulungu wa Isiraeli zimene Yerobowamu anachita.+
16 Iye adzasiya Isiraeli+ chifukwa cha machimo amene Yerobowamu anachita, ndiponso amene anachimwitsa nawo Isiraeli.”+
30 Izi zinachitika chifukwa cha machimo amene Yerobowamu anachita,+ ndiponso amene anachimwitsa nawo Isiraeli, komanso chifukwa cha zinthu zokwiyitsa Yehova Mulungu wa Isiraeli zimene Yerobowamu anachita.+