1 Mafumu 13:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Atatero, mneneri wokalambayo anakaika mtembowo m’manda ake. Ndipo anapitiriza kumulira+ kuti: “Kalanga ine, m’bale wanga!” 1 Mafumu 13:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Atamuika m’manda, mneneri wokalambayo anauza ana ake kuti: “Ine ndikadzamwalira mudzandiike m’manda amene taika munthu wa Mulungu woona uja. Mudzaike mafupa anga pambali pa mafupa ake,+
30 Atatero, mneneri wokalambayo anakaika mtembowo m’manda ake. Ndipo anapitiriza kumulira+ kuti: “Kalanga ine, m’bale wanga!”
31 Atamuika m’manda, mneneri wokalambayo anauza ana ake kuti: “Ine ndikadzamwalira mudzandiike m’manda amene taika munthu wa Mulungu woona uja. Mudzaike mafupa anga pambali pa mafupa ake,+