2 Mafumu 23:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Choncho iye anati: “Musiyeni apume.+ Musalole aliyense kudodometsa mafupa ake.” Chotero iwo sanakhudze mafupa akewo limodzi ndi mafupa a mneneri+ amene anachokera ku Samariya. Aheberi 11:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Mwa chikhulupiriro, Yosefe atayandikira mapeto a moyo wake, anatchula za kusamuka+ kwa ana a Isiraeli, ndipo anapereka lamulo lokhudza mafupa ake.+
18 Choncho iye anati: “Musiyeni apume.+ Musalole aliyense kudodometsa mafupa ake.” Chotero iwo sanakhudze mafupa akewo limodzi ndi mafupa a mneneri+ amene anachokera ku Samariya.
22 Mwa chikhulupiriro, Yosefe atayandikira mapeto a moyo wake, anatchula za kusamuka+ kwa ana a Isiraeli, ndipo anapereka lamulo lokhudza mafupa ake.+