1 Mafumu 13:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Tsopano panali munthu+ wa Mulungu amene anatumidwa+ ndi Yehova kuchokera ku Yuda kupita ku Beteli. Kumeneko iye anapeza Yerobowamu ataimirira pambali pa guwa lansembe+ kuti afukize nsembe yautsi.+
13 Tsopano panali munthu+ wa Mulungu amene anatumidwa+ ndi Yehova kuchokera ku Yuda kupita ku Beteli. Kumeneko iye anapeza Yerobowamu ataimirira pambali pa guwa lansembe+ kuti afukize nsembe yautsi.+