1 Mafumu 12:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Yerobowamu anayamba kumanga akachisi m’malo okwezeka.+ Ndiyeno anasankha anthu wamba, anthu amene sanali ana a Levi, n’kuwaika kuti akhale ansembe.+ 1 Mafumu 13:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 chifukwa mawu a Yehova oitanira tsoka amene munthu wa Mulungu uja ananena kwa guwa lansembe+ limene lili ku Beteli, ndi kwa akachisi onse a m’malo okwezeka+ amene ali m’mizinda ya ku Samariya,+ ndithu adzakwaniritsidwa.”+
31 Yerobowamu anayamba kumanga akachisi m’malo okwezeka.+ Ndiyeno anasankha anthu wamba, anthu amene sanali ana a Levi, n’kuwaika kuti akhale ansembe.+
32 chifukwa mawu a Yehova oitanira tsoka amene munthu wa Mulungu uja ananena kwa guwa lansembe+ limene lili ku Beteli, ndi kwa akachisi onse a m’malo okwezeka+ amene ali m’mizinda ya ku Samariya,+ ndithu adzakwaniritsidwa.”+