1 Mafumu 13:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 chifukwa mawu a Yehova oitanira tsoka amene munthu wa Mulungu uja ananena kwa guwa lansembe+ limene lili ku Beteli, ndi kwa akachisi onse a m’malo okwezeka+ amene ali m’mizinda ya ku Samariya,+ ndithu adzakwaniritsidwa.”+ Ezekieli 16:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Unamanga malo ako okwerawo pamphambano iliyonse ya msewu+ ndipo unaipitsa kukongola kwako.+ Unayamba kukhanyulira munthu aliyense wodutsa+ n’kumachulukitsa zochita zako zauhule.+
32 chifukwa mawu a Yehova oitanira tsoka amene munthu wa Mulungu uja ananena kwa guwa lansembe+ limene lili ku Beteli, ndi kwa akachisi onse a m’malo okwezeka+ amene ali m’mizinda ya ku Samariya,+ ndithu adzakwaniritsidwa.”+
25 Unamanga malo ako okwerawo pamphambano iliyonse ya msewu+ ndipo unaipitsa kukongola kwako.+ Unayamba kukhanyulira munthu aliyense wodutsa+ n’kumachulukitsa zochita zako zauhule.+