2 Mafumu 21:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iye anachita zoipa pamaso pa Yehova,+ mogwirizana ndi zonyansa za mitundu+ imene Yehova anaithamangitsa pamaso pa ana a Isiraeli. 2 Mafumu 21:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Iye anapitiriza kuyenda m’njira zonse zimene bambo ake anayendamo,+ ndipo anapitiriza kutumikira mafano onyansa+ amene bambo ake anawatumikira, n’kumawagwadira. 3 Yohane 11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Wokondedwa, usamatsanzire zinthu zoipa koma uzitsanzira zabwino.+ Munthu amene amachita zabwino ndi wochokera kwa Mulungu.+ Koma wochita zoipa sadziwa Mulungu.+
2 Iye anachita zoipa pamaso pa Yehova,+ mogwirizana ndi zonyansa za mitundu+ imene Yehova anaithamangitsa pamaso pa ana a Isiraeli.
21 Iye anapitiriza kuyenda m’njira zonse zimene bambo ake anayendamo,+ ndipo anapitiriza kutumikira mafano onyansa+ amene bambo ake anawatumikira, n’kumawagwadira.
11 Wokondedwa, usamatsanzire zinthu zoipa koma uzitsanzira zabwino.+ Munthu amene amachita zabwino ndi wochokera kwa Mulungu.+ Koma wochita zoipa sadziwa Mulungu.+