2 Mafumu 23:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Kenako Farao Neko+ anamanga+ Yehoahazi ku Ribila+ m’dziko la Hamati, kuti asalamulirenso ku Yerusalemu. Ndiyeno Farao Neko analamula+ dzikolo kuti lim’patse matalente 100 a siliva+ ndi talente imodzi ya golide.+
33 Kenako Farao Neko+ anamanga+ Yehoahazi ku Ribila+ m’dziko la Hamati, kuti asalamulirenso ku Yerusalemu. Ndiyeno Farao Neko analamula+ dzikolo kuti lim’patse matalente 100 a siliva+ ndi talente imodzi ya golide.+