Aroma 13:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Munthu aliyense azimvera+ olamulira akuluakulu,+ chifukwa palibe ulamuliro+ umene ungakhalepo kupatulapo ngati Mulungu waulola.+ Olamulira amene alipowa ali m’malo awo osiyanasiyana+ mololedwa ndi Mulungu.+ Aroma 13:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Perekani kwa onse zimene amafuna. Amene amafuna msonkho, m’patseni msonkho.+ Amene amafuna ndalama ya chiphaso, m’patseni ndalama ya chiphaso. Amene amafuna kuopedwa, muopeni.+ Amene amafuna kupatsidwa ulemu, m’patseni ulemu wake.+
13 Munthu aliyense azimvera+ olamulira akuluakulu,+ chifukwa palibe ulamuliro+ umene ungakhalepo kupatulapo ngati Mulungu waulola.+ Olamulira amene alipowa ali m’malo awo osiyanasiyana+ mololedwa ndi Mulungu.+
7 Perekani kwa onse zimene amafuna. Amene amafuna msonkho, m’patseni msonkho.+ Amene amafuna ndalama ya chiphaso, m’patseni ndalama ya chiphaso. Amene amafuna kuopedwa, muopeni.+ Amene amafuna kupatsidwa ulemu, m’patseni ulemu wake.+