2 Mafumu 21:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Choncho iye anamanganso malo okwezeka amene Hezekiya bambo ake anachotsa.+ Anamanga maguwa ansembe a Baala n’kumanga mzati wopatulika, monga momwe Ahabu+ mfumu ya Isiraeli anachitira. Iye anayambanso kugwadira+ khamu lonse la zinthu zakuthambo,+ n’kumazitumikira.+ 2 Mafumu 21:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Manase anatentha* mwana wake wamwamuna pamoto,+ ndipo ankachita zamatsenga,+ ankawombeza,*+ ndiponso anaika anthu olankhula ndi mizimu ndi olosera+ zam’tsogolo. Iye anachita zinthu zambiri zoipa pamaso pa Yehova ndiponso zomukwiyitsa.
3 Choncho iye anamanganso malo okwezeka amene Hezekiya bambo ake anachotsa.+ Anamanga maguwa ansembe a Baala n’kumanga mzati wopatulika, monga momwe Ahabu+ mfumu ya Isiraeli anachitira. Iye anayambanso kugwadira+ khamu lonse la zinthu zakuthambo,+ n’kumazitumikira.+
6 Manase anatentha* mwana wake wamwamuna pamoto,+ ndipo ankachita zamatsenga,+ ankawombeza,*+ ndiponso anaika anthu olankhula ndi mizimu ndi olosera+ zam’tsogolo. Iye anachita zinthu zambiri zoipa pamaso pa Yehova ndiponso zomukwiyitsa.