Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mafumu 18:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Hezekiya ndiye anachotsa malo okwezeka,+ kugwetsa zipilala zopatulika,+ ndi kudula mzati wopatulika.+ Iye anaphwanyaphwanya njoka yamkuwa+ imene Mose anapanga,+ chifukwa pofika masiku amenewo, ana a Isiraeli anakhala akufukiza nsembe+ yautsi kwa njoka yamkuwayo, ndipo inkatchedwa fano la njoka yamkuwa.+

  • 2 Mafumu 18:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Ngati amuna inu mungandiuze kuti, ‘Tikudalira+ Yehova Mulungu wathu,’+ kodi si iye amene Hezekiya+ wam’chotsera malo ake okwezeka+ ndi maguwa ake ansembe, n’kuuza Yuda ndi Yerusalemu kuti, ‘Muzigwada patsogolo pa guwa lansembe ili, la ku Yerusalemu’?”’+

  • 2 Mbiri 32:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Kodi si Hezekiya yemweyo amene anachotsa malo ake okwezeka+ ndi maguwa ake ansembe+ kenako n’kuuza anthu a ku Yuda ndi ku Yerusalemu kuti: “Muziwerama+ pamaso pa guwa lansembe limodzi lokha+ ndipo nsembe yautsi muzifukiza pamenepo”?+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena