Genesis 40:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pakapita masiku atatu, Farao akutulutsa. Adzakubwezera ndithu pa ntchito yako yakale,+ yoperekera chikho kwa mfumuyo.+
13 Pakapita masiku atatu, Farao akutulutsa. Adzakubwezera ndithu pa ntchito yako yakale,+ yoperekera chikho kwa mfumuyo.+