Genesis 40:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Farao anabwezeradi pa ntchito mkulu wa operekera chikho uja,+ moti anapitiriza ntchito yake yoperekera chikho kwa Farao. Genesis 41:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Zimene anamasulirazo n’zimene zinachitikadi. Ineyo ndinabwezeretsedwa pa ntchito,+ koma mnzangayo anapachikidwa.”+ Yeremiya 52:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Kenako, m’chaka cha 37 cha ukapolo wa Yehoyakini+ mfumu ya Yuda, m’mwezi wa 12, pa tsiku la 25 la mweziwo, chaka chimene Evili-merodaki mfumu ya Babulo anakhala mfumu, iye anakomera mtima Yehoyakini mfumu ya Yuda ndi kumutulutsa m’ndende.+
21 Farao anabwezeradi pa ntchito mkulu wa operekera chikho uja,+ moti anapitiriza ntchito yake yoperekera chikho kwa Farao.
13 Zimene anamasulirazo n’zimene zinachitikadi. Ineyo ndinabwezeretsedwa pa ntchito,+ koma mnzangayo anapachikidwa.”+
31 Kenako, m’chaka cha 37 cha ukapolo wa Yehoyakini+ mfumu ya Yuda, m’mwezi wa 12, pa tsiku la 25 la mweziwo, chaka chimene Evili-merodaki mfumu ya Babulo anakhala mfumu, iye anakomera mtima Yehoyakini mfumu ya Yuda ndi kumutulutsa m’ndende.+