Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mafumu 24:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Yehoyakini+ anali ndi zaka 18 pamene anayamba kulamulira, ndipo analamulira miyezi itatu ku Yerusalemu.+ Mayi ake anali a ku Yerusalemu ndipo dzina lawo linali Nehusita mwana wa Elinatani.

  • 2 Mafumu 25:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 M’chaka cha 37 cha ukapolo wa Yehoyakini+ mfumu ya Yuda, m’mwezi wa 12, pa tsiku la 27 la mweziwo, chaka chimene Evili-merodaki+ mfumu ya Babulo anakhala mfumu, iye anakomera mtima+ Yehoyakini mfumu ya Yuda ndi kumutulutsa m’ndende.

  • Yeremiya 24:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Ndiyeno Yehova anandisonyeza madengu awiri a nkhuyu amene anali patsogolo pa kachisi wa Yehova. Anandisonyeza zimenezi Nebukadirezara mfumu ya Babulo atatenga Yekoniya+ mwana wa Yehoyakimu,+ mfumu ya Yuda, pamodzi ndi akalonga a Yuda, amisiri+ ndi omanga makoma achitetezo kuchokera ku Yerusalemu kupita nawo ku ukapolo ku Babulo.+

  • Yeremiya 37:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 37 Ndiyeno Mfumu Zedekiya+ mwana wa Yosiya,+ amene Nebukadirezara mfumu ya Babulo anamuika kukhala mfumu m’dziko la Yuda,+ anayamba kulamulira m’malo mwa Koniya+ mwana wa Yehoyakimu.+

  • Mateyu 1:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Yosiya+ anabereka Yekoniya+ ndi abale ake pa nthawi imene Ayuda anatengedwa kupita ku Babulo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena