2 Mafumu 24:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pomalizira pake Yehoyakimu anagona pamodzi ndi makolo ake,+ ndipo Yehoyakini mwana wake anayamba kulamulira m’malo mwake. 1 Mbiri 3:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Mwana wa Yehoyakimu anali Yekoniya.+ Yekoniya anabereka Zedekiya. Yeremiya 22:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 “‘Pali ine, Mulungu wamoyo,’ watero Yehova, ‘ngakhale iwe Koniya+ mwana wa Yehoyakimu,+ mfumu ya Yuda, utakhala mphete yodindira+ kudzanja langa lamanja, ndidzakuvula!+
6 Pomalizira pake Yehoyakimu anagona pamodzi ndi makolo ake,+ ndipo Yehoyakini mwana wake anayamba kulamulira m’malo mwake.
24 “‘Pali ine, Mulungu wamoyo,’ watero Yehova, ‘ngakhale iwe Koniya+ mwana wa Yehoyakimu,+ mfumu ya Yuda, utakhala mphete yodindira+ kudzanja langa lamanja, ndidzakuvula!+