2 Mafumu 24:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pomalizira pake Yehoyakimu anagona pamodzi ndi makolo ake,+ ndipo Yehoyakini mwana wake anayamba kulamulira m’malo mwake. 2 Mafumu 25:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 M’chaka cha 37 cha ukapolo wa Yehoyakini+ mfumu ya Yuda, m’mwezi wa 12, pa tsiku la 27 la mweziwo, chaka chimene Evili-merodaki+ mfumu ya Babulo anakhala mfumu, iye anakomera mtima+ Yehoyakini mfumu ya Yuda ndi kumutulutsa m’ndende. Mateyu 1:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Yosiya+ anabereka Yekoniya+ ndi abale ake pa nthawi imene Ayuda anatengedwa kupita ku Babulo.+
6 Pomalizira pake Yehoyakimu anagona pamodzi ndi makolo ake,+ ndipo Yehoyakini mwana wake anayamba kulamulira m’malo mwake.
27 M’chaka cha 37 cha ukapolo wa Yehoyakini+ mfumu ya Yuda, m’mwezi wa 12, pa tsiku la 27 la mweziwo, chaka chimene Evili-merodaki+ mfumu ya Babulo anakhala mfumu, iye anakomera mtima+ Yehoyakini mfumu ya Yuda ndi kumutulutsa m’ndende.