1 Mbiri 3:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ana a Yosiya anali awa: woyamba Yohanani, wachiwiri Yehoyakimu,+ wachitatu Zedekiya,+ ndipo wachinayi anali Salumu. 1 Mbiri 3:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Mwana wa Yehoyakimu anali Yekoniya.+ Yekoniya anabereka Zedekiya. Yeremiya 28:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 “‘Ndipo Yekoniya+ mwana wa Yehoyakimu,+ mfumu ya Yuda, ndiponso anthu onse a mu Yuda amene anatengedwa kupita ku ukapolo ku Babulo+ ndiwabwezeretsa kuno, pakuti ndithyola goli+ la mfumu ya Babulo,’ watero Yehova.”
15 Ana a Yosiya anali awa: woyamba Yohanani, wachiwiri Yehoyakimu,+ wachitatu Zedekiya,+ ndipo wachinayi anali Salumu.
4 “‘Ndipo Yekoniya+ mwana wa Yehoyakimu,+ mfumu ya Yuda, ndiponso anthu onse a mu Yuda amene anatengedwa kupita ku ukapolo ku Babulo+ ndiwabwezeretsa kuno, pakuti ndithyola goli+ la mfumu ya Babulo,’ watero Yehova.”