2 Mafumu 23:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Yehoyakimu anali ndi zaka 25+ pamene anayamba kulamulira, ndipo analamulira zaka 11 ku Yerusalemu.+ Mayi ake anali a ku Ruma, ndipo dzina lawo linali Zebida mwana wa Pedaya. 2 Mafumu 24:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pomalizira pake Yehoyakimu anagona pamodzi ndi makolo ake,+ ndipo Yehoyakini mwana wake anayamba kulamulira m’malo mwake.
36 Yehoyakimu anali ndi zaka 25+ pamene anayamba kulamulira, ndipo analamulira zaka 11 ku Yerusalemu.+ Mayi ake anali a ku Ruma, ndipo dzina lawo linali Zebida mwana wa Pedaya.
6 Pomalizira pake Yehoyakimu anagona pamodzi ndi makolo ake,+ ndipo Yehoyakini mwana wake anayamba kulamulira m’malo mwake.