2 Mafumu 24:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pomalizira pake Yehoyakimu anagona pamodzi ndi makolo ake,+ ndipo Yehoyakini mwana wake anayamba kulamulira m’malo mwake. Danieli 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 M’chaka chachitatu cha ufumu wa Yehoyakimu+ mfumu ya Yuda, Nebukadinezara mfumu ya Babulo anabwera ku Yerusalemu ndipo anazungulira mzindawo.+
6 Pomalizira pake Yehoyakimu anagona pamodzi ndi makolo ake,+ ndipo Yehoyakini mwana wake anayamba kulamulira m’malo mwake.
1 M’chaka chachitatu cha ufumu wa Yehoyakimu+ mfumu ya Yuda, Nebukadinezara mfumu ya Babulo anabwera ku Yerusalemu ndipo anazungulira mzindawo.+