Maliro 4:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ngakhale amayi, amene amakhala achifundo, afika pophika ana awo ndi manja awo.+Anawo akhala ngati chakudya chotonthoza anthu pa nthawi ya kuwonongedwa kwa mwana wamkazi wa anthu anga.+
10 Ngakhale amayi, amene amakhala achifundo, afika pophika ana awo ndi manja awo.+Anawo akhala ngati chakudya chotonthoza anthu pa nthawi ya kuwonongedwa kwa mwana wamkazi wa anthu anga.+