Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 28:55
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 55 kuti asagawireko aliyense wa iwo mnofu uliwonse wa ana ake aamuna amene adzawadya. Adzatero poona kuti alibiretu china chilichonse, chifukwa cha zovuta ndi nsautso zimene mdani wanu adzakupanikizani nazo m’mizinda yanu yonse.+

  • Deuteronomo 28:57
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 57 Adzayang’ananso ndi diso loipa zotuluka m’mimba mwake pambuyo pobereka komanso ana ake aamuna amene iye anabereka,+ chifukwa adzawadya mseri pokhala wosowa chilichonse chifukwa cha zovuta ndi nsautso zimene mdani wanu adzakupanikizani nazo m’mizinda yanu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena