1 Mafumu 12:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Choncho mfumuyo inakambirana ndi anthu ena+ n’kupanga ana awiri a ng’ombe agolide.+ Itatero inauza anthuwo kuti: “N’zovuta kwambiri kwa inu kuti muzipita ku Yerusalemu. Nayu Mulungu wanu+ Aisiraeli inu, amene anakutulutsani m’dziko la Iguputo.”+ 1 Mafumu 16:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Kuwonjezera apo, anamanga guwa lansembe la Baala m’kachisi+ wa Baala amene iye anamanga ku Samariya.
28 Choncho mfumuyo inakambirana ndi anthu ena+ n’kupanga ana awiri a ng’ombe agolide.+ Itatero inauza anthuwo kuti: “N’zovuta kwambiri kwa inu kuti muzipita ku Yerusalemu. Nayu Mulungu wanu+ Aisiraeli inu, amene anakutulutsani m’dziko la Iguputo.”+
32 Kuwonjezera apo, anamanga guwa lansembe la Baala m’kachisi+ wa Baala amene iye anamanga ku Samariya.