1 Mafumu 21:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Komanso ponena za Yezebeli, Yehova wanena kuti, ‘Agalu adzamudya Yezebeli m’munda wa ku Yezereeli.+
23 Komanso ponena za Yezebeli, Yehova wanena kuti, ‘Agalu adzamudya Yezebeli m’munda wa ku Yezereeli.+