2 Mafumu 9:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Yezebeli adzadyedwa ndi agalu+ m’munda wa ku Yezereeli, ndipo palibe amene adzamuike m’manda.’” Mtumikiyo atamaliza kunena zimenezi, anatsegula chitseko n’kuthawa.+ 2 Mafumu 9:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Atapita kuti akam’tenge kukamuika m’manda, sanapezepo chilichonse. Iwo anangopezapo mutu, mapazi, ndi zikhatho zake. + Salimo 7:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Mavuto ake adzabwerera pamutu pake,+Ndipo chiwawa chake chidzatsikira paliwombo pake.+
10 Yezebeli adzadyedwa ndi agalu+ m’munda wa ku Yezereeli, ndipo palibe amene adzamuike m’manda.’” Mtumikiyo atamaliza kunena zimenezi, anatsegula chitseko n’kuthawa.+
35 Atapita kuti akam’tenge kukamuika m’manda, sanapezepo chilichonse. Iwo anangopezapo mutu, mapazi, ndi zikhatho zake. +