1 Mafumu 21:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Choncho Yezebeli analemba makalata+ m’dzina la Ahabu n’kuwadinda ndi chidindo cha Ahabu.+ Kenako anatumiza makalatawo kwa akulu+ ndi anthu olemekezeka amene anali kukhala mumzinda umodzi ndi Naboti.
8 Choncho Yezebeli analemba makalata+ m’dzina la Ahabu n’kuwadinda ndi chidindo cha Ahabu.+ Kenako anatumiza makalatawo kwa akulu+ ndi anthu olemekezeka amene anali kukhala mumzinda umodzi ndi Naboti.