2 Mafumu 9:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Kenako Yehu anafika ku Yezereeli,+ ndipo Yezebeli+ anamva zimenezo. Yezebeliyo anadzikongoletsa podzipaka utoto+ wakuda m’maso mwake n’kukongoletsanso tsitsi lake mochititsa kaso.+ Atatero anakaima pawindo n’kumayang’ana kunja.+
30 Kenako Yehu anafika ku Yezereeli,+ ndipo Yezebeli+ anamva zimenezo. Yezebeliyo anadzikongoletsa podzipaka utoto+ wakuda m’maso mwake n’kukongoletsanso tsitsi lake mochititsa kaso.+ Atatero anakaima pawindo n’kumayang’ana kunja.+