Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 32:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Pamenepo iye anawauza kuti: “Yehova Mulungu wa Isiraeli wanena kuti, ‘Aliyense wa inu amange lupanga lake m’chiuno mwake. Ndiyeno mudutse mkati mwa msasa ndi kuyenda mobwerezabwereza, kuchoka pachipata china kufika pachipata china, ndipo aliyense wa inu aphe m’bale wake, mnzake ndi mnzake wapamtima.’”+

  • Deuteronomo 13:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 “M’bale wako, amene ndi mwana wamwamuna wa mayi ako, kapena mwana wako wamwamuna, mwana wako wamkazi, mkazi wako wokondedwa kapena bwenzi lako lapamtima,+ akayesa kukupatutsa mwamseri pokuuza kuti, ‘Tiye tikatumikire milungu ina,’+ milungu imene iwe kapena makolo ako sanaidziwe,

  • Deuteronomo 13:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 usavomereze zofuna zake kapena kumumvera.+ Diso lako lisamumvere chifundo ndipo usamumvere chisoni+ kapena kum’bisa kuti um’teteze.

  • Ezekieli 9:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Ndiyeno iye anauza amuna ena aja ine ndikumva, kuti: “M’tsatireni ameneyu. Muyendeyende mumzindamo n’kumapha anthu. Diso lanu lisamve chisoni ndipo inuyo musachite chifundo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena