Ezekieli 29:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 “‘Ndamupatsa dziko la Iguputo monga chipukutamisozi pa utumiki wake umene anachita pomenyana ndi Turo, chifukwa iwo anachita zimene ine ndinali kufuna,’+ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.
20 “‘Ndamupatsa dziko la Iguputo monga chipukutamisozi pa utumiki wake umene anachita pomenyana ndi Turo, chifukwa iwo anachita zimene ine ndinali kufuna,’+ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.