Ezekieli 30:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pa tsikulo, amithenga ochokera kwa ine adzakwera zombo kuti akaopseze Itiyopiya yemwe ndi wodzidalira.+ Itiyopiya adzamva ululu woopsa pa tsiku limene Iguputo adzawonongedwe, pakuti tsikulo lidzafika ndithu.’+ Ezekieli 30:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 “Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Ndidzawononga khamu la ku Iguputo pogwiritsa ntchito dzanja la Nebukadirezara, mfumu ya Babulo.+
9 Pa tsikulo, amithenga ochokera kwa ine adzakwera zombo kuti akaopseze Itiyopiya yemwe ndi wodzidalira.+ Itiyopiya adzamva ululu woopsa pa tsiku limene Iguputo adzawonongedwe, pakuti tsikulo lidzafika ndithu.’+
10 “Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Ndidzawononga khamu la ku Iguputo pogwiritsa ntchito dzanja la Nebukadirezara, mfumu ya Babulo.+