Ezekieli 29:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ndimupatsa dziko la Iguputo monga chipukutamisozi pa ntchito imene anagwira pomenyana ndi Turo, chifukwa iwo anachita zimene ine ndinkafuna,’+ akutero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa. Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 29:20 Nsanja ya Olonda,8/1/2007, tsa. 9
20 Ndimupatsa dziko la Iguputo monga chipukutamisozi pa ntchito imene anagwira pomenyana ndi Turo, chifukwa iwo anachita zimene ine ndinkafuna,’+ akutero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.