Ezekieli 29:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 “‘Ndamupatsa dziko la Iguputo monga chipukutamisozi pa utumiki wake umene anachita pomenyana ndi Turo, chifukwa iwo anachita zimene ine ndinali kufuna,’+ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa. Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 29:20 Nsanja ya Olonda,8/1/2007, tsa. 9
20 “‘Ndamupatsa dziko la Iguputo monga chipukutamisozi pa utumiki wake umene anachita pomenyana ndi Turo, chifukwa iwo anachita zimene ine ndinali kufuna,’+ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.