2 Mafumu 11:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Gawo lina limodzi mwa magawo atatu a inu lidzakhale pachipata+ chotchedwa Maziko, ndipo gawo linanso limodzi mwa magawo atatu a inu lidzakhale pachipata kumbuyo kwa asilikali othamanga. Muzidzasinthana kulondera mosamala nyumbayo.+ Salimo 84:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pakuti kukhala tsiku limodzi m’mabwalo anu n’kwabwino kuposa kukhala masiku 1,000 kwina.+Ndasankha kuima pakhomo la nyumba ya Mulungu wanga+Kuposa kukhala m’mahema a anthu oipa.+
6 Gawo lina limodzi mwa magawo atatu a inu lidzakhale pachipata+ chotchedwa Maziko, ndipo gawo linanso limodzi mwa magawo atatu a inu lidzakhale pachipata kumbuyo kwa asilikali othamanga. Muzidzasinthana kulondera mosamala nyumbayo.+
10 Pakuti kukhala tsiku limodzi m’mabwalo anu n’kwabwino kuposa kukhala masiku 1,000 kwina.+Ndasankha kuima pakhomo la nyumba ya Mulungu wanga+Kuposa kukhala m’mahema a anthu oipa.+