Yoswa 4:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Pa tsikuli, Yehova anachititsa Yoswa kukhala wamkulu m’maso mwa Aisiraeli onse,+ ndipo anayamba kumuopa monga mmene anaopera Mose masiku onse a moyo wake.+ Aroma 12:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pokonda abale,+ khalani ndi chikondi chenicheni pakati panu. Posonyezana ulemu,+ khalani patsogolo.
14 Pa tsikuli, Yehova anachititsa Yoswa kukhala wamkulu m’maso mwa Aisiraeli onse,+ ndipo anayamba kumuopa monga mmene anaopera Mose masiku onse a moyo wake.+
10 Pokonda abale,+ khalani ndi chikondi chenicheni pakati panu. Posonyezana ulemu,+ khalani patsogolo.