2 Mafumu 10:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Pomalizira pake Yehu anagona pamodzi ndi makolo ake,+ ndipo anamuika m’manda ku Samariya. Kenako Yehoahazi+ mwana wake anayamba kulamulira m’malo mwake.
35 Pomalizira pake Yehu anagona pamodzi ndi makolo ake,+ ndipo anamuika m’manda ku Samariya. Kenako Yehoahazi+ mwana wake anayamba kulamulira m’malo mwake.