2 Mafumu 14:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Tsopano Amaziya anatumiza amithenga kwa Yehoasi mwana wa Yehoahazi mwana wa Yehu mfumu ya Isiraeli, ndi uthenga wakuti: “Bwera tidzamenyane.”+
8 Tsopano Amaziya anatumiza amithenga kwa Yehoasi mwana wa Yehoahazi mwana wa Yehu mfumu ya Isiraeli, ndi uthenga wakuti: “Bwera tidzamenyane.”+