-
2 Samueli 2:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Pamapeto pake Abineri anauza Yowabu kuti: “Bwanji anyamata athu anyamuke ndipo amenyane tione.” Poyankha, Yowabu anati: “Chabwino, zitero.”
-