-
2 Mbiri 25:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Yehoasi mfumu ya Isiraeli atamva anamuyankha Amaziya mfumu ya Yuda kuti:+ “Chitsamba chaminga cha ku Lebanoni chinatumiza uthenga kwa mtengo wa mkungudza wa ku Lebanoni,+ wakuti, ‘Ndipatse mwana wako wamkazi kuti mwana wanga wamwamuna amukwatire.’+ Koma nyama yakuthengo+ ya ku Lebanoni inadutsa pamenepo n’kupondaponda chitsamba chaminga chija.
-